PAC ikumana ndi APM
Public Affairs Committee (PAC) yalimbikitsa zipani kuti zizichita kampeni ya mtendere pamene dziko la Malawi likuyembekezeka kuchititsa zisankho zapatatu pa 16 September chaka chino. Izi zadziwika Lachinayi pamene PAC idakumana ndi mtsogoleri wa chipani chotsutsa… ...