Otsatira DPP adadwa ndi kukwezedwa udindo komanso kusunthidwa kwa gavanala wa Mangochi Central
Otsatira chipani chotsutsa cha Democratic Progressive Party (DPP) asonyeza kudabwa ndi kukhudzidwa ndi kusunthidwa kwa gavanala woyang’anira ntchito za chipanichi m’chigawo cha pakati m’boma la Mangochi, a Sanudi Sande.