Ine za gospel zanuzo ayi – wasambwadza Peter Sambo
Woyimba Peter Sambo sanafune kubisa za ku khosi koma kulavula chichewa ponena kuti iye siwoyimba nyimbo zauzimu ndipo wasambwadza kuti oyimba nyimbo zauzimu ambiri ndi mimbulu koma amadzionetsa ngati nkhosa. “Ndilekeni ine ndili phee! Sindikupanga… ...