Makhonsolo alibe ndalama – Ngwale
Phungu wa ku Nyumba ya Malamulo dera la Chiradzulu West Mathews Ngwale, wadandaula kuti aphungu akayima kupempha zitukuko ku ma unduna, unduna ukakhala opanda mayankho umawabwezera nkhani ya chitukukocho kuti aphungu apite nayo ku khonsolo… ...