Gaba wasumira timu yake, akufuna K82 miliyoni
Katswiri womwetsa zigoli mu timu ya dziko lino Flames, Gabadinho Mhango, watengera timu yake ya Marumo Gallants ku khothi pomwe akufuna ndalama zoposa K82 miliyoni kwacha kamba kogwiritsa ntchito zithuzi zake. Malingana ndi tsamba la… ...