• Thursday April, 2025

Mphatso Khutcha Richard

Mphatso Khutcha Richard

Articles by Mphatso Khutcha Richard

Nkhondo idakalipo mu EPL
Malawi News

Nkhondo idakalipo mu EPL

Timu ya Manchester United yasokelera m'nkhalango ya Nottingham pomwe pa nthawi yomwe imakatulukira kuti njira ndi iyi, wawo wakale Anthony Elanga anali atawapanga kale chipongwe mkati mwa nkhalangoyi kuti asawone njira mu mphindi zisanu zoyambilira… ...

FAM yatchetcha ma bwalo asanu nthawi yothaitha
Malawi News

FAM yatchetcha ma bwalo asanu nthawi yothaitha

Bungwe loyendetsa mpira wa miyendo m'dziko muno la Football Association of Malawi (FAM) kudzera mu komiti yake, lakana kuvomeleza ndi kuika pa mndandanda ma bwalo asanu mwa ma bwalo oti ayambe kugwiritsidwa ntchito pomwe masewelo… ...

Silver Strikers yadya Wanderers kuti itenge 2025 NBS Bank Charity Shield
Malawi News

Silver Strikers yadya Wanderers kuti itenge 2025 NBS Bank Charity Shield

Timu ya Silver Strikers yaswa akatswiri a Castel Challenge Cup a Mighty Wanderers mochita kuchokera kumbuyo kukafanana mphamvu 2-2 zomwe zinakusila awiriwa ku ma penate mu mpikisano wa NBS Bank Charity Shield dzulo pa bwalo… ...

Milandu ina ndi yongofunika kukambirana – Gangata
Malawi News

Milandu ina ndi yongofunika kukambirana – Gangata

Wachiwiri kwa mtsogoleri mchipani cha Democratic Progressive (DPP) mchigawo cha pakati, a Alfred Gangata, ati mchitidwe omangana wawonjeza pomwe ati amanganso Commissioner wa apolisi chifukwa cha paint. Iwo ati commissioner wa apolisi monga wamkulu samayenera… ...

Gaba ndi Petro atsala pomwe Flames yanyamuka wa ku Tunisia
Malawi News

Gaba ndi Petro atsala pomwe Flames yanyamuka wa ku Tunisia

Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya the Flames yanyamuka ulendo wokakumana ndi Tunisia m'masewelo olimbirana malo ku mpikisano wa 2026 FIFA World Cup kudzera pa bwalo la ndenge la Kamuzu international mu… ...

Usi akubweleranso ku Namibia
Malawi News

Usi akubweleranso ku Namibia

Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi lero anyamuka ulendo opitanso mdziko la Namibia kukakhala nawo pa mwambo olumbilitsa mtsogoleri watsopano wa dzikolo a Netumbo Nandi-Ndaitwah. Malinga ndi chikalata chochokera ku unduna wowona… ...

Manchester United yaswa Leicester City
Malawi News

Manchester United yaswa Leicester City

Manchester United ya Ruben Amorim yayamba kuyenda kukwera mtunda tsopano pomwe pano ili pa nambala 13 ndi ma points ake 37 pomwe yaswa Leicester City 3-0 pa bwalo King Power, mu chikho cha English Premier… ...

Liverpool zake zada
Malawi News

Liverpool zake zada

Anyamata awiri a timu ya Liverpool Darwin Nunez ndi Curtis Jones ndi omwe anambwandilitsa ma penate awo m'manja mwa goloboyi wa PSG Gianluigi Donnarumma pa bwalo la Anfield usiku wathawu mu mpikisano wa UEFA Champions… ...

EPL yayaka moto
Malawi News

EPL yayaka moto

Loto la timu ya Arsenal likusanduka loto la chumba pomwe chomwe ikufuna mu English Premier League (EPL) chikuoneka chawatelera kuposa mlamba. Izi zili delo kutsatira mpata wa ma points 13 omwe ulipo tsopano kuti agwirane… ...

Akong’onthananso lero
Malawi News

Akong’onthananso lero

Masewelo ena aakulu lero lamulungu 4:00 masanawa pomwe Manchester City chindunji ndi makosana a Liverpool omwe pano akuyenda mapewa m'mwamba kutsogola ndi ma points awo 61, mu chikho chachikulu ku England cha English Premier League… ...