Mzika ya dziko lino ikufuna K300 miliyoni kuchokera ku Immigration ngati chipepeso
Mzika ina ya dziko lino, a Stevens Prince Thengo yati ikufuna nthambi yowona zolowa komanso kutuluka m'dziko muno (Department of Immigration and Citizenship Services) imupatse ndalama yokwana K300 miliyoni ngati chipukuta misonzi. Malingana ndi chikalata… ...