• Monday June, 2025

Malawi24 Reporter

Malawi24 Reporter

Articles by Malawi24 Reporter

Katundu akupitilira kukwera pa msika
Malawi News

Katundu akupitilira kukwera pa msika

A Malawi akungoyenera kuvala zilimbe pomwe katundu osiyanasiyana akupitilira kukwera mtengo tsiku ndi tsiku. Katundu wambiri yemwe aMalawi amagwiritsa ntchito akunka nakwera ndipo anthu ambiri m'dziko muno akukhalira kudandaula. Katundu monga mafuta ophikira pano akwera… ...

Mutharika’s Comeback Bid Gathers Steam
Malawi News

Mutharika’s Comeback Bid Gathers Steam

Former President of the Republic of Malawi who is also Democratic Progressive Party (DPP) president, Arthur Peter Muntharika says the return to proven leadership has started and it is progressing very well. Writing on his… ...

Alekeni aMalawi asankhe yemwe akufuna – Kachamba
Malawi News

Alekeni aMalawi asankhe yemwe akufuna – Kachamba

M'modzi mwa ochita malonda m'dziko muno, Kondwani Kachamba walakhurapo za bilu yomwe ikufuna kupita ku Nyumba ya Malamulo yoletsa munthu yemwe wafika zaka 80 kuyimira pa udindo wa m'tsogoleri wa dziko. Polankhura pa tsamba lawo… ...

Ana atatu afa atamira mu damu ku Dowa
Malawi News

Ana atatu afa atamira mu damu ku Dowa

Ana atatu omwe ndi a banja limodzi amwalira atamira pomwe amakasewera kufupi ndi damu lina m’boma la Dowa Malingana ndi m'neneri wa polisi ya Mponela, a Macpatson Msadala, izi zachitika m'mudzi wa Chakomba mdera la… ...

Mulungu sanandiyike pampandowu kuti ndilephere – Chakwera
Malawi News

Mulungu sanandiyike pampandowu kuti ndilephere – Chakwera

Pomwe tangotsala ndi miyezi isanu ndi umodzi kuti tipite ku chisankho chapatatu, m'tsogoleri wa dziko lino, Lazarus Chakwera wati Mulungu sanalakwitse kumuyika pampando wotsogolera dziko lino. Ndipo sanamuyike kuti alaphere kuyendetsa dziko. Chakwera analankhura izi… ...

White South Africans Decline Trump’s Refugee Offer
Malawi News

White South Africans Decline Trump’s Refugee Offer

Groups representing South Africa's white minority have declined President Donald Trump's offer of refugee status and resettlement in the United States. Trump's plan was part of a broader response to South Africa's land reform policy,… ...

Zipani ziwiri zikuluzikulu zinandipempha kuti ndikhale runningmate ine ndidakana – Bushiri
Malawi News

Zipani ziwiri zikuluzikulu zinandipempha kuti ndikhale runningmate ine ndidakana – Bushiri

Mtumiki Shepherd Bushiri wati zipani ziwiri zikuluzikulu m'dziko muno zinamupeza ndikumupempha kuti akhale wachiwiri kwa otsogolera zipanizo (running mate), koma iye anakanitsitsa kuti sakufuna kupanga zimenezo. Iwo afotokoza izi mu macheza awo ndi kanema wa… ...

Karonga District Council unveils harmonized grievance redressing mechanism
Malawi News

Karonga District Council unveils harmonized grievance redressing mechanism

Karonga District Council has introduced a harmonized Grievance Redressing Mechanism (GRM) to stakeholders and civil society organizations, aiming to establish a standardized procedure for addressing misunderstandings within the district. Speaking during the District Executive Committee… ...

Ndinamangidwa ndi kuzunzidwa chifukwa chogula ndege – watero M’neneri Bushiri
Malawi News

Ndinamangidwa ndi kuzunzidwa chifukwa chogula ndege – watero M’neneri Bushiri

M'neneri Shepherd Bushiri wati kugula kwa ndege ndi chimodzi mwa zifukwa zomwe dziko la South Africa lidamumangira pamodzi ndi mkazi wake ponena kuti sizimagwirizana ndi msinkhu wake. Iwo afotokoza izi mu gawo loyamba la macheza… ...

Kagame Warns Ramaphosa: Rwanda Ready for Confrontation with South Africa
Malawi News

Kagame Warns Ramaphosa: Rwanda Ready for Confrontation with South Africa

Accuses SADC of Aiding DRC Government, Denies RDF Links to M23 Rebels Rwandan President Paul Kagame has issued a fierce warning, declaring that Rwanda is ready for a confrontation with South Africa "any day." This… ...