• Saturday January, 2025

Archangel Nzangaya

Archangel Nzangaya

Articles by Archangel Nzangaya

Bullets yafa ndi imodzi pomwe Wanderers yasaina Kamwendo
Malawi News

Bullets yafa ndi imodzi pomwe Wanderers yasaina Kamwendo

Pomwe timu ya FCB Nyasa Big Bullets inali itapeleka kale K3 miliyoni ndipo imadikira kuti iwonetse kugulu katswiri wosewera kutsogolo mu timu ya Premier Bet Dedza Dynamos, Promise Kamwendo, osewerayu watikitira kontalakiti ku Mighty Mukuru… ...

Mwana ali pa ndandanda okaphedwa ku Somaliland
Malawi News

Mwana ali pa ndandanda okaphedwa ku Somaliland

Zina ukamva kamba anga mwala: Mwana wa nzika yothawa kwawo yemwenso sanakwane zaka 18, ali pandandanda okanyongedwa m’dziko la Somaliland kamba kopha m'modzi mwa anthu omwe ankafuna kumupanga chiwembu. Pa 11 February chaka chino, bwalo… ...

PRISAM Takes Step to Elevate Early Childhood Education
Malawi News

PRISAM Takes Step to Elevate Early Childhood Education

The Private Schools Association of Malawi (PRISAM) has made a significant contribution to advancing early childhood education by sponsoring the training of all teachers from private nursery schools. On Friday, the association signed a Memorandum… ...

Unraveling the Mysteries: ‘Sinister Bonds’ Movie Continues with Episode Two
Malawi News

Unraveling the Mysteries: ‘Sinister Bonds’ Movie Continues with Episode Two

After a thrilling premiere that left audiences on the edge of their seats, the wait is finally over as episode two of the gripping Malawian movie, “Sinister Bonds,” is finally out.  The first episode left… ...

GOtv Malawi Slams Customers with Price Hikes
Malawi News

GOtv Malawi Slams Customers with Price Hikes

GOtv customers in Malawi will need to dig deeper into their pockets as the company has dealt them a blow by effecting a significant price hike across all its packages, citing economic pressures as the justification… ...

UDF Delays Next Week’s Elective Convention
Malawi News

UDF Delays Next Week’s Elective Convention

The United Democratic Front (UDF) has postponed its National Elective Conference, originally scheduled for August 3, 2024. UDF Acting Publicity Secretary Yusuf Mwawa, through a statement, announced that the party's National Executive Committee decided to… ...

Nzika ya ku Britain yabedwa ku Lilongwe
Malawi News

Nzika ya ku Britain yabedwa ku Lilongwe

Apolisi munzinda wa Lilongwe atsimikiza kuti nzika ya m’dziko la Britain ya zaka 26 yabedwa ndi anthu osadziwika pomwe imachokera ku mapemphero Lolemba masana.  Malingana ndi ofalitsa nkhani za polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu,… ...

Dziko lapita kwa agalu – watelo Kalindo
Malawi News

Dziko lapita kwa agalu – watelo Kalindo

Omenyera ufulu wa anthu Bon Kalindo yemwe wavekedwa unyolo mowilikiza pakatipa wati zithu zambiri ndizosokonekera m'dziko muno kamba koti dziko lino linapita kwa agalu. Poyankhula mu pologalamu ya padera yomwe yaulutsidwa pa wayilesi ya Zodiak… ...

Abale sakudziwabe komwe kuli Chiyanjano Mbeza
Malawi News

Abale sakudziwabe komwe kuli Chiyanjano Mbeza

Patadutsa maola oposa 24 apolisi chimangileni mkozi wa nyimbo, Chiyanjano Mbeza pa mlandu omwe sukudziwika, achibale ake ati mpaka pano sakudziwabe polisi yomwe m'bale wawoyu akusungidwa. Mbeza yemwe amajambula nyimbo munzinda wa Blantyre, anamangidwa madzulo… ...

Lekani kuononga misonkho pomayenda m’misika, tsitsani mitengo ya zinthu – wadzudzura Mneneri David Mbewe
Malawi News

Lekani kuononga misonkho pomayenda m’misika, tsitsani mitengo ya zinthu – wadzudzura Mneneri David Mbewe

Mtsogoleri wa chipani cha Liberation for Economic Freedom (LEF) M'neneri David Mbewe, wauza wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Michael Usi kuti asiye kuyendera misika ponena kuti akuononga misonkho yomwe itha kugwira ntchito zina zotukura… ...