Afa atawombedwa ndi mphenzi
Mtsikana wa zaka 15, Enifa George, wafa atawombedwa ndi mphenzi m'mudzi mwa Amoni 1, mfumu yaikulu Nsamala ku Balaka. Inspector Gladson M'bumpha yemwe amayankhulira nkhani apolisi m'bomali watsimikiza izi poyankhula ndi Malawi24. A M'bumpha ati… ...