Mkhalakale pa uwulutsi pa wayilesi, Lucius Chikuni, wamwalira
Katswiri komanso mkhalakale pa uwulutsi wa pa wayilesi, a Lucius Chikuni, amwalira pa chipatala cha Mwaiwathu munzinda wa Blantyre. Chikuni yemwe amadziwika bwino chifukwa cha mawu ake okhathamira, wamwalira m'bandakucha wa lero Lolemba pa 10… ...